-
Maliko 13:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Atakhala pansi mʼphiri la Maolivi, kachisi akuonekera bwino, Petulo, Yakobo, Yohane ndi Andireya anamufunsa ali paokha kuti:
-