Maliko 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa.+ Koma amene adzapirire* mpaka mapeto+ ndi amene adzapulumuke.+
13 Ndipo anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa.+ Koma amene adzapirire* mpaka mapeto+ ndi amene adzapulumuke.+