Maliko 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa kudzabwera anthu onamizira kuti ndi Khristu ndiponso aneneri abodza+ ndipo adzachita zizindikiro komanso zodabwitsa kuti ngati nʼkotheka, adzasocheretse osankhidwawo.
22 Chifukwa kudzabwera anthu onamizira kuti ndi Khristu ndiponso aneneri abodza+ ndipo adzachita zizindikiro komanso zodabwitsa kuti ngati nʼkotheka, adzasocheretse osankhidwawo.