Maliko 13:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kumwamba ndi dziko lapansi zidzachoka,+ koma mawu anga adzakhalapo mpaka kalekale.+