Maliko 13:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kunena za tsiku limenelo kapena ola lake, palibe amene akudziwa, ngakhale angelo kumwamba kapenanso Mwana, kupatulapo Atate wokha.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:32 Kukambitsirana, tsa. 396
32 Kunena za tsiku limenelo kapena ola lake, palibe amene akudziwa, ngakhale angelo kumwamba kapenanso Mwana, kupatulapo Atate wokha.+