Maliko 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Khalani maso, khalani tcheru,+ chifukwa simukudziwa kuti nthawi yoikidwiratu idzafika liti.+