Maliko 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndi zofanana ndi munthu amene akupita kudziko lina, amene wasiya nyumba mʼmanja mwa akapolo ake,+ aliyense pantchito yake, nʼkulamula mlonda wapageti kuti azikhala tcheru.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:34 Nsanja ya Olonda,3/1/2004, ptsa. 10-11
34 Ndi zofanana ndi munthu amene akupita kudziko lina, amene wasiya nyumba mʼmanja mwa akapolo ake,+ aliyense pantchito yake, nʼkulamula mlonda wapageti kuti azikhala tcheru.+