Maliko 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano kunangotsala masiku awiri kuti Pasika+ ndi Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa+ zichitike. Ndipo ansembe aakulu ndi alembi ankafunafuna njira yoti agwiritse ntchito pogwira* Yesu mochenjera nʼkumupha.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 266 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, ptsa. 8-9
14 Tsopano kunangotsala masiku awiri kuti Pasika+ ndi Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa+ zichitike. Ndipo ansembe aakulu ndi alembi ankafunafuna njira yoti agwiritse ntchito pogwira* Yesu mochenjera nʼkumupha.+