-
Maliko 14:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Pa nthawi imene Yesu anali ku Betaniya mʼnyumba mwa Simoni wakhate, kunafika mayi wina ali ndi botolo lopangidwa ndi mwala wa alabasitala la mafuta onunkhira. Mafutawa anali nado weniweni ndipo anali okwera mtengo kwambiri. Iye anatsegula botolo la alabasitala lija mochita kuswa, nʼkuyamba kuthira mafutawo mʼmutu mwa Yesu.+
-