Maliko 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mafuta onunkhirawatu akanatha kugulitsidwa ndalama zoposa madinari* 300 ndipo ndalamazo zikanaperekedwa kwa anthu osauka!” Choncho iwo anakhumudwa kwambiri ndi mayiyo.* Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:5 Nsanja ya Olonda,5/1/2008, tsa. 31
5 Mafuta onunkhirawatu akanatha kugulitsidwa ndalama zoposa madinari* 300 ndipo ndalamazo zikanaperekedwa kwa anthu osauka!” Choncho iwo anakhumudwa kwambiri ndi mayiyo.*