Maliko 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndithu ndikukuuzani, kulikonse kumene uthenga wabwino udzalalikidwe padziko lonse,+ anthu azidzanena zimene mayiyu wachita kuti azidzamukumbukira.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:9 Nsanja ya Olonda,4/15/1999, tsa. 16
9 Ndithu ndikukuuzani, kulikonse kumene uthenga wabwino udzalalikidwe padziko lonse,+ anthu azidzanena zimene mayiyu wachita kuti azidzamukumbukira.”+