Maliko 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa tsiku loyamba la chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa,+ pamene mwamwambo ankapereka nsembe nyama ya Pasika,+ ophunzira ake anamufunsa kuti: “Kodi mukufuna tikakukonzereni kuti malo odyerako Pasika?”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:12 Yesu—Ndi Njira, tsa. 267 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 9
12 Pa tsiku loyamba la chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa,+ pamene mwamwambo ankapereka nsembe nyama ya Pasika,+ ophunzira ake anamufunsa kuti: “Kodi mukufuna tikakukonzereni kuti malo odyerako Pasika?”+