Maliko 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno Yesu anatuma awiri mwa ophunzira akewo nʼkuwauza kuti: “Pitani mumzinda ndipo mwamuna wina akakumana nanu atasenza mtsuko wa madzi. Mukamutsatire,+
13 Ndiyeno Yesu anatuma awiri mwa ophunzira akewo nʼkuwauza kuti: “Pitani mumzinda ndipo mwamuna wina akakumana nanu atasenza mtsuko wa madzi. Mukamutsatire,+