-
Maliko 14:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Choncho ophunzirawo anapita nʼkulowa mumzinda ndipo zinachitikadi ndendende mmene iye anawauzira. Ndipo kumeneko anakonza zinthu zonse zofunika pa Pasika.
-