Maliko 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo atakhala patebulo nʼkumadya chakudya, Yesu anati: “Ndithu ndikukuuzani, mmodzi wa inu, amene akudya nane limodzi, andipereka.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:18 Yesu—Ndi Njira, tsa. 270 Nsanja ya Olonda,7/1/1990, tsa. 8
18 Ndipo atakhala patebulo nʼkumadya chakudya, Yesu anati: “Ndithu ndikukuuzani, mmodzi wa inu, amene akudya nane limodzi, andipereka.”+