Maliko 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa nʼkundisiya ndekha, chifukwa Malemba amanena kuti: ‘Ndidzapha mʼbusa+ ndipo nkhosa zidzabalalika.’+
27 Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa nʼkundisiya ndekha, chifukwa Malemba amanena kuti: ‘Ndidzapha mʼbusa+ ndipo nkhosa zidzabalalika.’+