Maliko 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma Petulo anayankha kuti: “Ngakhale ena onse atathawa nʼkukusiyani, ine ndekha sindidzathawa.”+