-
Maliko 14:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Choncho atapita patsogolo pangʼono, anagwada mpaka nkhope yake pansi ndipo anayamba kupemphera kuti ngati zikanatheka, ola limeneli limupitirire.
-