Maliko 14:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Atatero anabwerera ndipo anawapeza akugona. Choncho anafunsa Petulo kuti: “Simoni, zoona ukugona? Kodi unalibe mphamvu kuti ukanakhalabe maso kwa ola limodzi?+
37 Atatero anabwerera ndipo anawapeza akugona. Choncho anafunsa Petulo kuti: “Simoni, zoona ukugona? Kodi unalibe mphamvu kuti ukanakhalabe maso kwa ola limodzi?+