Maliko 14:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Anabweranso kachitatu nʼkuwauza kuti: “Zoona nthawi ngati ino mukugona ndi kupumula? Basi! Nthawi yakwana!+ Taonani! Mwana wa munthu akuperekedwa mʼmanja mwa anthu ochimwa.
41 Anabweranso kachitatu nʼkuwauza kuti: “Zoona nthawi ngati ino mukugona ndi kupumula? Basi! Nthawi yakwana!+ Taonani! Mwana wa munthu akuperekedwa mʼmanja mwa anthu ochimwa.