Maliko 14:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Apa nʼkuti womuperekayu atawapatsa chizindikiro chakuti: “Amene ndikamukise* ndi yemweyo, mukamugwire nʼkupita naye ndipo muonetsetse kuti asathawe.” Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:44 Yesu—Ndi Njira, tsa. 284 Nsanja ya Olonda,10/15/1990, tsa. 8
44 Apa nʼkuti womuperekayu atawapatsa chizindikiro chakuti: “Amene ndikamukise* ndi yemweyo, mukamugwire nʼkupita naye ndipo muonetsetse kuti asathawe.”