-
Maliko 14:51Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
51 Koma mnyamata wina amene anangofunda nsalu yabwino popanda chovala china mkati, anayamba kumutsatira chapafupi ndipo anthuwo anayesa kuti amugwire.
-