Maliko 14:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Koma Petulo ankamutsatira ali chapatali ndithu, mpaka anafika mʼbwalo lapanyumba ya mkulu wa ansembeyo. Petuloyo anakhala pansi limodzi ndi antchito amʼnyumbamo nʼkumawotha moto walawilawi.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:54 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288 Tsanzirani, tsa. 200 Nsanja ya Olonda,4/1/2010, tsa. 2311/15/1990, tsa. 8
54 Koma Petulo ankamutsatira ali chapatali ndithu, mpaka anafika mʼbwalo lapanyumba ya mkulu wa ansembeyo. Petuloyo anakhala pansi limodzi ndi antchito amʼnyumbamo nʼkumawotha moto walawilawi.+
14:54 Yesu—Ndi Njira, tsa. 288 Tsanzirani, tsa. 200 Nsanja ya Olonda,4/1/2010, tsa. 2311/15/1990, tsa. 8