Maliko 14:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Anthu ambiri ankapereka umboni wabodza kuti amunamizire mlandu,+ koma maumboni awowo ankatsutsana.
56 Anthu ambiri ankapereka umboni wabodza kuti amunamizire mlandu,+ koma maumboni awowo ankatsutsana.