Maliko 14:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Ndipo ena anayamba kumulavulira,+ kumuphimba nkhope nʼkumamukhoma nkhonya. Iwo ankamuuza kuti: “Losera!” Atamuwomba mbama, asilikali apakhoti anamutenga.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:65 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 14
65 Ndipo ena anayamba kumulavulira,+ kumuphimba nkhope nʼkumamukhoma nkhonya. Iwo ankamuuza kuti: “Losera!” Atamuwomba mbama, asilikali apakhoti anamutenga.+