Maliko 14:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Koma iye anakana kuti: “Sindikumudziwa ngakhale pangʼono ameneyo ndipo sindikumvetsa zimene ukunena.” Atatero anatuluka panja nʼkupita pageti.* Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:68 Nsanja ya Olonda,11/15/1990, tsa. 8
68 Koma iye anakana kuti: “Sindikumudziwa ngakhale pangʼono ameneyo ndipo sindikumvetsa zimene ukunena.” Atatero anatuluka panja nʼkupita pageti.*