Maliko 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Pilato anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe Mfumu ya Ayuda?”+ Iye anayankha kuti: “Zili choncho, monga mmene mwanenera.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:2 Yesu—Ndi Njira, tsa. 291 Nsanja ya Olonda,6/1/2011, tsa. 18
2 Choncho Pilato anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe Mfumu ya Ayuda?”+ Iye anayankha kuti: “Zili choncho, monga mmene mwanenera.”+