-
Maliko 15:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Pa nthawiyo munthu wina dzina lake Baraba anali mundende limodzi ndi anthu oukira boma. Iwo anapha munthu pa nthawi imene ankaukira boma.
-