Maliko 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atatero, pofuna kukwaniritsa zofuna za anthuwo, Pilato anawamasulira Baraba. Ndiyeno analamula kuti Yesu akwapulidwe+ kenako anamupereka kuti akamuphe pomupachika pamtengo.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:15 Yesu—Ndi Njira, tsa. 294 Nsanja ya Olonda,1/1/1991, tsa. 9
15 Atatero, pofuna kukwaniritsa zofuna za anthuwo, Pilato anawamasulira Baraba. Ndiyeno analamula kuti Yesu akwapulidwe+ kenako anamupereka kuti akamuphe pomupachika pamtengo.+