Maliko 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Asilikali anamutenga nʼkupita naye mʼbwalo lapanyumba ya bwanamkubwa. Kumeneko anasonkhanitsa gulu lonse la asilikali.+
16 Asilikali anamutenga nʼkupita naye mʼbwalo lapanyumba ya bwanamkubwa. Kumeneko anasonkhanitsa gulu lonse la asilikali.+