Maliko 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atamaliza kumunyozako, anamuvula chovala chapepo chija nʼkumuveka malaya ake akunja ndipo anatuluka naye kupita kukamukhomerera pamtengo.+
20 Atamaliza kumunyozako, anamuvula chovala chapepo chija nʼkumuveka malaya ake akunja ndipo anatuluka naye kupita kukamukhomerera pamtengo.+