Maliko 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso iwo anakakamiza munthu wina amene ankangodutsa dzina lake Simoni wa ku Kurene kuti asenze mtengo wake wozunzikirapo.* Iyeyu ankachokera kudera lakumidzi ndipo anali bambo wa Alekizanda ndi Rufu.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:21 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 296-297 Nsanja ya Olonda,7/15/1992, tsa. 6
21 Komanso iwo anakakamiza munthu wina amene ankangodutsa dzina lake Simoni wa ku Kurene kuti asenze mtengo wake wozunzikirapo.* Iyeyu ankachokera kudera lakumidzi ndipo anali bambo wa Alekizanda ndi Rufu.+