Maliko 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo anamukhomerera pamtengo nʼkugawana malaya ake akunja pochita maere pa malayawo, kuti aone chimene munthu aliyense angatenge.+
24 Ndipo anamukhomerera pamtengo nʼkugawana malaya ake akunja pochita maere pa malayawo, kuti aone chimene munthu aliyense angatenge.+