Maliko 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anthu amene ankadutsa pafupi ankanena mawu onyoza Yesu ndipo ankapukusa mitu yawo+ nʼkumanena kuti: “Iwe amene unkanena kuti ungathe kugwetsa kachisi nʼkumumanga mʼmasiku atatu,+
29 Anthu amene ankadutsa pafupi ankanena mawu onyoza Yesu ndipo ankapukusa mitu yawo+ nʼkumanena kuti: “Iwe amene unkanena kuti ungathe kugwetsa kachisi nʼkumumanga mʼmasiku atatu,+