Maliko 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopanotu Khristu, Mfumu ya Isiraeli, itsike pamtengo wozunzikirapowo,* kuti ife tione ndi kukhulupirira.”+ Nawonso achifwamba amene anapachikidwa naye limodzi aja ankamunyoza.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:32 Nsanja ya Olonda,8/15/1989, ptsa. 10-11
32 Tsopanotu Khristu, Mfumu ya Isiraeli, itsike pamtengo wozunzikirapowo,* kuti ife tione ndi kukhulupirira.”+ Nawonso achifwamba amene anapachikidwa naye limodzi aja ankamunyoza.+