Maliko 15:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako wina anathamanga kukaviika siponji muvinyo wowawasa ndipo anaiika kubango nʼkumupatsa kuti amwe.+ Iye ananena kuti: “Mulekeni! Tione ngati Eliya angabwere kudzamutsitsa.”
36 Kenako wina anathamanga kukaviika siponji muvinyo wowawasa ndipo anaiika kubango nʼkumupatsa kuti amwe.+ Iye ananena kuti: “Mulekeni! Tione ngati Eliya angabwere kudzamutsitsa.”