Maliko 15:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndiyeno nsalu yotchinga yamʼnyumba yopatulika+ inangʼambika pakati kuchokera pamwamba mpaka pansi.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:38 Yesu—Ndi Njira, tsa. 301 Nsanja ya Olonda,2/15/1991, ptsa. 8-9
38 Ndiyeno nsalu yotchinga yamʼnyumba yopatulika+ inangʼambika pakati kuchokera pamwamba mpaka pansi.+