Maliko 15:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Tsopano, mtsogoleri wa asilikali amene anaimirira chapafupi moyangʼanizana ndi Yesu, ataona zimene zinachitika pa nthawi imene anatsirizika, ananena kuti: “Ndithudi munthu uyu analidi Mwana wa Mulungu.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:39 Yesu—Ndi Njira, tsa. 301 Nsanja ya Olonda,2/15/1991, tsa. 9
39 Tsopano, mtsogoleri wa asilikali amene anaimirira chapafupi moyangʼanizana ndi Yesu, ataona zimene zinachitika pa nthawi imene anatsirizika, ananena kuti: “Ndithudi munthu uyu analidi Mwana wa Mulungu.”+