Maliko 15:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Panalinso azimayi amene ankaonerera chapatali ndithu. Ena mwa iwo anali Mariya wa ku Magadala, Mariya mayi a Yakobo Wamngʼono ndi Yose komanso panali Salome,+
40 Panalinso azimayi amene ankaonerera chapatali ndithu. Ena mwa iwo anali Mariya wa ku Magadala, Mariya mayi a Yakobo Wamngʼono ndi Yose komanso panali Salome,+