Maliko 15:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 amene ankayenda naye limodzi nʼkumamutumikira+ pa nthawi imene anali ku Galileya. Panalinso azimayi ena ambiri amene anabwera naye limodzi kuchokera ku Yerusalemu. Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:41 Nsanja ya Olonda,8/15/2015, tsa. 30
41 amene ankayenda naye limodzi nʼkumamutumikira+ pa nthawi imene anali ku Galileya. Panalinso azimayi ena ambiri amene anabwera naye limodzi kuchokera ku Yerusalemu.