Maliko 15:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 kunabwera Yosefe wa ku Arimateya, munthu wodziwika wa mʼKhoti Lalikulu la Ayuda, amenenso ankayembekezera Ufumu wa Mulungu. Iye anapita molimba mtima kwa Pilato kukapempha mtembo wa Yesu.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:43 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, ptsa. 17-19
43 kunabwera Yosefe wa ku Arimateya, munthu wodziwika wa mʼKhoti Lalikulu la Ayuda, amenenso ankayembekezera Ufumu wa Mulungu. Iye anapita molimba mtima kwa Pilato kukapempha mtembo wa Yesu.+