-
Maliko 15:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 Koma Pilato ankakayikira ngati anali atamwalira kale. Choncho anaitanitsa mtsogoleri wa asilikali nʼkumufunsa ngatidi Yesu anali atamwalira kale.
-