Maliko 15:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndiyeno Yosefe atagula nsalu yabwino kwambiri nʼkumutsitsa, anamukulunga ndi nsaluyo nʼkumuika mʼmanda*+ amene anawasema mʼthanthwe. Kenako anagubuduza chimwala nʼkutseka pakhomo la mandawo.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:46 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, tsa. 20 Nsanja ya Olonda,3/1/2013, tsa. 8
46 Ndiyeno Yosefe atagula nsalu yabwino kwambiri nʼkumutsitsa, anamukulunga ndi nsaluyo nʼkumuika mʼmanda*+ amene anawasema mʼthanthwe. Kenako anagubuduza chimwala nʼkutseka pakhomo la mandawo.+