Maliko 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsiku la Sabata+ litatha, Mariya wa ku Magadala, Mariya+ mayi wa Yakobo ndi Salome anagula zonunkhiritsa kuti akapake thupi la Yesu.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:1 Nsanja ya Olonda,3/1/2013, tsa. 83/1/1991, tsa. 9
16 Tsiku la Sabata+ litatha, Mariya wa ku Magadala, Mariya+ mayi wa Yakobo ndi Salome anagula zonunkhiritsa kuti akapake thupi la Yesu.+