Maliko 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo atatuluka mʼmandawo anayamba kuthawa akunjenjemera komanso kunthunthumira kwambiri. Ndipo sanauze munthu aliyense zimene zinachitikazo chifukwa anali ndi mantha.*+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:8 Nsanja ya Olonda,9/1/2014, tsa. 15
8 Iwo atatuluka mʼmandawo anayamba kuthawa akunjenjemera komanso kunthunthumira kwambiri. Ndipo sanauze munthu aliyense zimene zinachitikazo chifukwa anali ndi mantha.*+