-
Luka 1:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndiyeno Zekariya anafunsa mngeloyo kuti: “Nditsimikiza bwanji zimenezi? Inetu ndine wokalamba ndipo mkazi wanganso ali ndi zaka zambiri.”
-
-
1. Kuwala Kwenikweni kwa DzikoMalifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu
-
-
Gabirieli ananeneratu za kubadwa kwa Yohane M’batizi (gnj 1 06:04–13:53)
-