-
Luka 1:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Ndipotu mʼbale wako Elizabeti, amene anthu amamunena kuti mkazi wosabereka, nayenso ndi woyembekezera ndipo adzabereka mwana wamwamuna mu ukalamba wake, moti uno ndi mwezi wake wa 6.
-
-
1. Kuwala Kwenikweni kwa DzikoMalifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu
-
-
Gabirieli ananeneratu za kubadwa kwa Yesu (gnj 1 13:52–18:26)
-