Luka 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho angelowo atachoka nʼkubwerera kumwamba, abusawo anayamba kuuzana kuti: “Tiyeni tipite ndithu ku Betelehemu kuti tikaone zimene zachitikazo, zimene Yehova* watidziwitsa.” 1. Kuwala Kwenikweni kwa Dziko Malifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu Abusa anapita kukhola la ng’ombe (gnj 1 41:41–43:53)
15 Choncho angelowo atachoka nʼkubwerera kumwamba, abusawo anayamba kuuzana kuti: “Tiyeni tipite ndithu ku Betelehemu kuti tikaone zimene zachitikazo, zimene Yehova* watidziwitsa.”