-
Luka 2:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Kenako abusa aja anabwerera, akulemekeza komanso kutamanda Mulungu chifukwa cha zonse zimene anamva ndi kuziona, mogwirizana ndi zimene anauzidwa.
-
-
1. Kuwala Kwenikweni kwa DzikoMalifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu
-
-
Abusa anapita kukhola la ng’ombe (gnj 1 41:41–43:53)
-