Luka 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kunalinso mneneri wamkazi, dzina lake Anna mwana wa Fanueli, wa fuko la Aseri. Mayi ameneyu anali wachikulire kwambiri ndipo anakhala ndi mwamuna wake zaka 7 zokha kuchokera pamene anakwatirana.* Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:36 Nsanja ya Olonda,5/15/1994, tsa. 26 1. Kuwala Kwenikweni kwa Dziko Malifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu Anna analankhula zokhudza mwanayo (gnj 1 48:52–50:21)
36 Kunalinso mneneri wamkazi, dzina lake Anna mwana wa Fanueli, wa fuko la Aseri. Mayi ameneyu anali wachikulire kwambiri ndipo anakhala ndi mwamuna wake zaka 7 zokha kuchokera pamene anakwatirana.*